Job 22:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amapulumutsa munthu wopanda mlandu, adzakupulumutsa iwenso ndi kulungama kwako.” Yobe
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzamasula ngakhale wopalamula, inde adzamasuka mwa kuyera kwa manja ako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzapulumutsa ngakhale munthu amene ndi wolakwa, ameneyo adzapulumutsidwa kudzera mʼkulungama kwako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzamasula ngakhale woparamula, Inde adzamasuka mwa kuyera kwa manja ako.