Job 22:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi nchifukwa choti umamuwopa, kuti azikudzudzula, kuti azifuna kukukokera ku mlandu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi akudzudzula, nadza nawe kumlandu, chifukwa cha kumuopa kwako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi nʼchifukwa choti umamuopa, kuti azikudzudzula, kuti azifuna kukukokera ku mlandu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi akudzudzula, nadza nawe kumlandu, Cifukwa ca kumuopa kwako?