Job 22:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Iwe unkaumiriza pachabe abale ako kuti apereke chikole, ndipo unkaŵalanda zovala zao, mpaka kuŵasiya ali ndi usiŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti wamtenga chikole kwa mbale wako wopanda chifukwa, ndi kuvula ausiwa zovala zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe unkawumiriza abale ako kuti akupatse chikole popanda chifukwa; umalanda anthu zovala zawo ndi kuwasiya amaliseche.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti wamtenga cikole kwa mbale wako wopanda cifukwa, Ndi kubvula ausiwa zobvala zao.