Job 22:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu otopa sudaŵapatse madzi akumwa, anthu anjala udaŵamana chakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sunampatsa wolema madzi amwe, ndi wanjala unammana chakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sunawapatse madzi anthu otopa, ndipo unawamana chakudya anthu anjala,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sunampatsa wolema madzi amwe, Ndi wanjala unammana cakudya.