Job 22:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha mphamvu zako udalanda dziko lalikulu, chifukwa cha kudzikonda udakhazikika m'menemo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma munthu mwini mphamvu, dziko ndi lake; ndi munthu wovomerezeka, anakhala momwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngakhale unali munthu wamphamvu, wokhala ndi malo akeake, munthu waulemu wake, wokhala mʼdzikomo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma munthu mwini mphamvu, dziko ndi lace; Ndi munthu wobvomerezeka, anakhala momwemo.