Job 22:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akazi amasiye udaŵachotsa opanda kanthu, ndipo ana amasiye udaŵapondereza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Unabweza akazi amasiye osawaninkha kanthu, ndi manja a ana amasiye anathyoledwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo akazi amasiye unawachotsa wopanda kanthu, ndipo unapondereza ana amasiye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Unabweza akazi amasiye osawaninkha kanthu, Ndi manja a ana amasiye anatyoledwa.