Job 23:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe Mulungu amadziŵa m'mene ndimayendera, akandiyesa adzapeza kuti ndine wangwiro ngati golide.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma adziwa njira ndilowayi; atandiyesa ndidzatuluka ngati golide.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Iye amadziwa mmene ndimayendera; Iyeyo akandiyesa adzandipeza kuti ndili ngati golide.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma adziwa njira ndilowayi; Atandiyesa ndidzaturuka ngati golidi.