Job 23:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindidapatuke kusiya malamulo ake. Ndasunga mau a pakamwa pake kupambana zofuna zanga zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sindinabwerera kusiya malamulo a pa milomo yake; ndasungitsa mau a pakamwa pake koposa lamulo langalanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sindinapatuke kusiya malamulo ochokera pakamwa pake; ndasunga mawu a pakamwa pake kupambana chakudya changa cha tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sindinabwerera kusiya malamulo a pa milomo yace; Ndasungitsa mau a pakamwa pace koposa lamulo langa langa.