Job 23:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zimene adatsimikiza kuti adzandichita, adzachitadi, ndipo amalingalira zambiri zoterezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti adzachita chondiikidwiratu; ndipo zambiri zotere zili ndi Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye amachita chimene watsimikiza kuti chindichitikire, ndipo malingaliro oterowa ali nawobe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti adzacita condiikidwiratu; Ndipo zambiri zotere ziri ndi Iye.