Job 23:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ndikuchita mantha kwambiri pamaso pake. Ndikaganiza za iyeyo, ndimaopa kwabasi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndiopsedwa pankhope pake; ndikalingirira, ndichita mantha ndi Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchifukwa chake ndikuchita mantha kwambiri pamaso pake; ndikamaganiza zonsezi ndimamuopa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndiopsedwa pankhope pace; Ndikalingirira, ndicita mantha ndi Iye.