Job 23:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu walefula mtima wanga. Mphambe wandiwopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Mulungu walefula mtima wanga, ndi Wamphamvuyonse wandiopsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu walefula mtima wanga; Wamphamvuzonse wandiopseza kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Mulungu walefula mtima wanga, Ndi Wamphamvuyonse wandiopsa.