Job 23:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wandichititsa mantha ndi Mulungu, osati mdima wa mavuto onse amene amandiphimbaŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza sindinalikhidwa usanafike mdimawo, ndipo sanandiphimbire nkhope yanga ndi mdima wa bii.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu sindinachititsidwe mantha ndi mdima, ndi mdima wandiweyani umene waphimba nkhope yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza sindinalikhidwa usanafike mdimawo, Ndipo sanandiphimbira nkhope yanga ndi mdima wa bii.