Job 23:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Leronso ndikudandaula kwambiri kwa Mulungu. Ngakhale ndikubuula, Mulungu akundilangiralangira ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Lero lomwe kudandaula kwanga kumawawa; kulanga kwanga kuposa kubuula kwanga m'kulemera kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Leronso kudandaula kwanga nʼkwakukulu kwambiri; Iye akundilanga kwambiri ngakhale ndi kubuwula.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Lero lomwe kudandaula kwanga kumawawa; Kulanga kwanga kuposa kubuula kwanga m'kulemera kwace.