Job 23:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ha, ndikadadziŵa kumene ndikadampeza Mulungu, kuti ndikafike mpaka komwe amakhalako!
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha! Ndikadadziwa kumene ndikampeza Mulungu, kuti ndifike kumpando wake!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikanangodziwa kumene ndikanamupeza Mulungu; ndikanangopita kumene amakhalako!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha! ndikadadziwa kumene ndikampeza Mulungu, Kuti ndifike ku mpando wace!