Job 23:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikadakamba mlandu wanga pamaso pake, bwenzi nditafotokoza zifukwa zanga zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikadalongosola mlandu wanga pamaso pake, ndikadadzaza m'kamwa mwanga ndi matsutsano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikanafotokoza mlandu wanga pamaso pake ndipo ndikanayankhula mawu odziteteza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikadalongosola mlandu wanga pamaso pace, Ndikadadzaza m'kamwa mwanga ndi matsutsano.