Job 23:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwenzi nditamva mau amene akadandiyankha, bwenzi nditamvetsa zimene akadandiwuza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndikadadziwa mau akadandiyankha ine, ndikadazindikira chimene akadanena nane.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikanadziwa mawu amene Iye akanandiyankha, ndi kulingalira bwino zimene akananena!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndikadadziwa mau akadandiyankha ine, Ndikadazindikira cimene akadanena nane.