Job 23:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi Mulungu akadalimbana nane ndi mphamvu zake? Ai, koma akadamva mau anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akadatsutsana nane kodi mwa mphamvu yake yaikulu? Iai, koma akadanditcherera khutu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Iye akanalimbana nane mwa mphamvu zake zazikulu? Ayi, Iye sakanayankhula zinthu zotsutsana nane.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akadatsutsana nane kodi mwa mphamvu yace yaikuru? Iai, koma akadandicherera khutu.