Job 24:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chifukwa chiyani Mphambe saikiratu nthaŵi yoti aweruze? Chifukwa chiyani amene ali olungama saŵaona masiku otero?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wamphamvuyonse alekeranji kuikiratu nyengo? Ndi iwo omdziwa alekeranji kudziwa masiku ake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Chifukwa chiyani Wamphamvuzonse sayikiratu nthawi yoti aweruze? Chifukwa chiyani iwo amene amadziwa Iyeyo amayembekezera pachabe masiku oterewa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wamphamvuyonse alekeranji kuikiratu nyengo? Ndi iwo omdziwa alekeranji kudziwa masiku ace?