Job 24:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amayenga mafuta a olivi m'minda ya anthu oipa, namapsinya mphesa, koma nkumamvabe ludzu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kati mwa malinga a iwo aja ayenga mafuta; aponda mphesa moponderamo, namva ludzu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amayenga mafuta a olivi mʼminda ya anthu oyipa; amapsinya mphesa, koma nʼkumamvabe ludzu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kati mwa malinga a iwo aja ayenga mafuta; Aponda mphesa moponderamo, namva ludzu.