Job 24:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene alikufa akubuula mumzindamo, anthu ovulala akulirira chithandizo. Komabe Mulungu sakusamalako mapemphero ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'mudzi waukulu anthu abuula alinkufa; ndi moyo wa iwo olasidwa ufuula; koma Mulungu sasamalira choipacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kubuwula kwa anthu amene akufa kumamveka kuchokera mu mzinda, anthu ovulala akulirira chithandizo. Koma Mulungu sakuyimba mlandu wina aliyense.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'mudzi waukuru anthu abuula alinkufa; Ndi moyo wa iwo olasidwa upfuula; Koma Mulungu sasamalira coipaco.