Job 24:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pali ena amene amakana kuŵala, safuna kuyenda m'kuŵalako, ndipo sadziŵa njira zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwo ndiwo amene apikisana nako kuunika, sadziwa njira zake, Sasunga mayendedwe ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pali ena amene amakana kuwala, amene safuna kuyenda mʼkuwalako kapena kukhala mʼnjira zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwo ndiwo amene apikisana nako kuunika, Sadziwa njira zace, Sasunga mayendedwe ace.