Job 24:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wopha anzake amadzuka usiku kuti aphe osauka ndi amphaŵi. Nthaŵi ya usiku ena amasanduka mbala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kukacha auka wambanda, napha wosauka ndi waumphawi; ndi usiku asanduka mbala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dzuwa likalowa, wopha anzake amadzuka ndipo amakapha osauka ndi amphawi; nthawi ya usiku iye amasanduka mbala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kukaca auka wambanda, napha wosauka ndi waumphawi; Ndi usiku asanduka mbala.