Job 24:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbala zimathyola nyumba usiku, masana zimadzitsekera, ndiye kuti zimapewa kuŵala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kuli mdima aboola nyumba, usana adzitsekera, osadziwa kuunika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbala zimathyola nyumba usiku, koma masana zimadzitsekera; izo zimathawa kuwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuli mdima aboola nyumba, Usana adzitsekera, Osadziwa kuunika.