Job 24:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onsewo kukada kwambiri, ndiye kuti kwaŵachera. Zoopsa za mdima woti goo ndiye bwenzi lao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti iwo onse auyesa m'mawa mthunzi wa imfa; pakuti adziwa zoopsa za mthunzi wa imfa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti kwa onsewa mdima wandiweyani ndiye kuti kwawachera. Iwo amachita ubale ndi zoopsa za mdima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti iwo onse auyesa m'mawa mthunzi wa imfa; Pakuti adziwa zoopsa za mthunzi wa imfa.