Job 24:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu woipa amatengedwa ndi madzi a chigumula. Minda yake njotembereredwa m'dziko lonse. Sapitako kukagwira ntchito ku minda yake yamphesa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atengedwa ngati choyandama pamadzi; gawo lao litembereredwa padziko; sadzalunjikanso njira ya minda yamphesa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Komatu iwowo ndi thovu loyandama pa madzi; minda yawo ndi yotembereredwa pa dzikolo kotero kuti palibe amene amapita ku minda ya mpesa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atengedwa ngati coyandama pamadzi; Gawo lao litembereredwa padziko; Sadzalunjikanso njira ya minda yamphesa.