Job 24:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Monga momwe amasungunukira matalala nkuloŵa pansi chifukwa cha fundira, ndimo m'mene munthu wochimwa adzatsikire ku dziko la akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chilala ndi dzuwa zitha madzi a chipale chofewa, momwemo manda achita nao ochimwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe kutentha ndi chilala zimasungunulira madzi owundana ndi momwemonso mmene manda amachotsera omwe achimwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cirala ndi dzuwa zitha madzi a cipale cofewa, Momwemo manda acita nao ocimwa.