Job 24:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena amasendeza malire, kuti akuze dziko lao, amalanda ziŵeto namakazidyetsa ku mabusa ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alipo akusendeza malire; alanda gulu la zoweta, nazidyetsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu amasuntha miyala ya mʼmalire, kuti akuze dziko lawo; amadyetsa ziweto zimene aba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alipo akusendeza malire; Alanda gulu la zoweta, nazidyetsa.