Job 24:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu amaononga anthu amphamvu. Anthuwo ngakhale atakhazikika, moyo wao ndi wosatsimikizika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu awakhalitsa amphamvu mwa mphamvu yake; iwo aukanso m'mene anayesa kuti sadzakhala ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mulungu amawononga munthu wamphamvu mwa mphamvu zake; ngakhale munthuyo atakhazikika, alibe chiyembekezo cha moyo wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu awakhalitsa amphamvu mwa mphamvu yace; Iwo aukanso m'mene anayesa kuti sadzakhala ndi moyo.