Job 24:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu angathe kumtchinjiriza munthu woipa ndi kumpatsa mtendere, koma amakhala akupenyetsetsa njira zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Awalola akhale osatekeseka, ndipo alimbikapo; koma maso ake ali pa njira zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu atha kuwalola kuti akhale mosatekeseka, koma amakhala akupenyetsetsa njira zawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Awalola akhale osatekeseka, ndipo alimbikapo; Koma maso ace ali pa njira zao.