Job 24:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndani angathe kukana kuti si momwemo? Kodi wina anganditsutse kuti mau angaŵa si oona?” Bilidadi
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ngati si kutero, anditsutsa ndani kuti ndili wabodza, ndi kuyesa mau anga opanda pake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati zimenezi sizoona, ndani angaonetse kuti ndine wabodza ndi kusandutsa mawu anga kukhala wopanda pake?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ngati si kutero, anditsutsa ndani kuti ndiri wabodza, Ndi kuyesa mau anga opanda pace?