Job 24:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amalanda abulu a ana amasiye, amalandanso ng'ombe za akazi amasiye, kuti zikhale chikole.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akankhizira kwao bulu wa amasiye, atenga ng'ombe ya mfedwa ikhale chikole.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amalanda abulu a ana amasiye ndipo amatenganso ngʼombe ya mkazi wamasiye ngati chikole.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akankhizira kwao buru wa amasiye, Atenga ng'ombe ya mfedwa ikhale cikole.