Job 24:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amphaŵiwo amakafunafuna chakudya ku chipululu ngati mbidzi. Kulibe kwina koti apezere ana ao chakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ngati mbidzi za m'chipululu atulukira kuntchito zao, nalawirira nkufuna chakudya; chipululu chiwaonetsera chakudya cha ana ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amphawiwo amakhala ngati mbidzi mʼchipululu, amayendayenda kufuna chakudya; dziko lowuma limapereka chakudya cha ana awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ngati mbidzi za m'cipululu Aturukira ku nchito zao, nalawirira nkufuna cakudya; Cipululu ciwaonetsera cakudya ca ana ao.