Job 24:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amakolola za m'minda ya eniake, amakunkha mphesa m'minda ya anthu oipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atema dzinthu zao m'munda; natola khunkha m'munda wampesa wa woipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amakolola za mʼminda ya eni ake, ndipo amakunkha mphesa mʼminda ya anthu oyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atema dzinthu zao m'munda; Natola khunkha m'munda wampesa wa woipa.