Job 24:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Palinso ena amene amatsomphola ana a masiye ku bele, ndipo amagwira ana a mmphaŵi kuti akhale chikole.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akwatula wamasiye kubere, natenga chikole chovala cha osauka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amatsomphola mwana wamasiye wa ku bere; ndipo amagwira mwana wakhanda wa mʼmphawi kuti akhale chikole.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akwatula wamasiye kubere, Natenga cikole cobvala ca osauka;