Job 25:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mulungu ali ndi ulamuliro wonse, ndipo anthu onse ayenera kumuwopa. Akusungitsa mtendere mu ufumu wake Kumwambamwambako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kulamulira ndi kuopsa kuli ndi Iye; achita mtendere pa zam'mwamba zake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ulamuliro ndi kuopsa ndi za Mulungu, Iye amakhazikitsa bata mu ufumu wake kumwambako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kulamulira ndi kuopsa kuti ndi Iye; Acita mtendere pa zam'mwamba zace.