Job 25:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati mwezi sutha kupereka kuŵala kwenikweni, ndipo ngati nyenyezi sizitha kunyezemira pamaso pake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ngakhale mwezi ulibe kuwala; ndi nyenyezi siziyera pamaso pake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mwezi sutha kuwala kwenikweni, ndipo nyenyezi sizitha kuwala pamaso pake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ngakhale mwezi ulibe kuwala; Ndi nyenyezi siziyera pamaso pace;