Job 25:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
nanji tsono munthu amene ali ngati mphutsi chabe, nanji mwana wa munthu amene ali ngati nyongolotsi yam'dothi?” Yobe
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kopambana kotani nanga munthu, ndiye mphutsi! Ndi wobadwa ndi munthu, ndiye nyongolotsi!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
nanji tsono munthu amene ali ngati mphutsi, mwana wa munthu amene ali ngati nyongolotsi!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kopambana kotani nanga munthu, ndiye mphutsi! Ndi wobadwa ndi munthu, ndiyo nyongolotsi!