Job 26:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mizati yochirikiza thambo lakumwamba imanjenjemera ndi mantha, imazizwa pakumva kudzudzula kwa Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mizati ya thambo injenjemera, ndi kudabwa pa kudzudzula kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mizati yochirikiza mitambo yakumwamba imanjenjemera, ndi kudabwa pa kudzudzula kwake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mizati ya thambo injenjemera, Ndi kudabwa pa kudzudzula kwace.