Job 26:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi mphamvu zake adatontholetsa nyanja, ndi nzeru zake adakantha chilombo cham'madzi chija cha Rahabu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa mphamvu yake agwetsa nyanja bata; ndipo mwa luntha lake akantha kudzikuza kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mphamvu zake anatontholetsa nyanja; ndi nzeru zake anakantha chirombo cha mʼmadzi chija chotchedwa Rahabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa mphamvu yace agwetsa nyanja bata; Ndipo mwa luntha lace akantha kudzikuza kwace.