Job 26:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndi mpweya mwake adayeretsa zamumlengalenga, ndi dzanja lake adapha chinjoka chothaŵa chija.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwa mzimu wake anyezimiritsa thambo; dzanja lake linapyoza njoka yothawayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi mpweya wake anayeretsa zamumlengalenga, dzanja lake linapha chinjoka chothawa chija.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwa mzimu wace anyezimiritsa thambo; Dzanja lace linapyoza njoka yothawayo.