Job 26:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi wandilangiza zabwino ine, munthu wopanda nzerune ngati? Kodi wandiwuza nzeru zambiri pamenepa ngati?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wampangira bwanji wopanda nzeruyu! Ndi kudziwitsa nzeru zenizeni mochuluka!
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wapereka malangizo kwa munthu amene alibe nzeru! Ndipotu waonetsadi nzeru zochuluka!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wampangira bwanji wopanda nzeruyu! Ndi kudziwitsa nzeru zeni zeni mocurukal