Job 26:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ndani adzamva mau akoŵa? Nanga udazitenga kuti zonsezi?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wafotokozera yani mau? Ndi mzimu wa yani unatuluka mwa iwe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi wakuthandiza ndani kuti uyankhule mawu awa? Ndipo ndi mzimu wa yani umene unayankhula pakamwa pako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wafotokozera yani mau? Ndi mzimu wa yani unaturuka mwa iwe?