Job 26:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mizimu ya anthu akufa ikunjenjemera pansi pa nthaka, zonse zokhala m'madzi pansipo zikuvutika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adafawo anjenjemera pansi pa madzi ndi zokhalamo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mizimu ya anthu akufa ikunjenjemera pansi pa madzi, ndi zonse zokhala mʼmadzimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adafawo anjenjemera Pansi pa madzi ndi zokhalamo,