Job 26:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko la anthu akufa ndi lapululu pamaso pa Mulungu, ndipo kumeneko sikuphimbika kwa Iye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kumanda kuli padagu pamaso pake, ndi kuchionongeko kusowa chophimbako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Dziko la anthu akufa ndi lapululu pamaso pa Mulungu; chiwonongeko ndi chosaphimbidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kumanda kuli padagu pamaso pace, Ndi kucionongeko kusowa cophimbako,