Job 26:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amasunga madzi ambiri m'mitambo yochindikira, koma mitamboyo sing'ambika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amanga madzi m'mitambo yake yochindikira; ndi mtambo sung'ambika pansi pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amasunga madzi ambiri mʼmitambo yake, koma mitamboyo siphulika chifukwa cha kulemera kwa madziwo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amanga madzi m'mitambo yace yocindikira; Ndi mtambo sung'ambika pansi pace,