Job 27:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithu, inu mwadziwonera nokha, nanga bwanji mukulankhula zachabe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, inu nonse munachiona; ndipo mugwidwa nazo zopanda pake chifukwa ninji?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwadzionera nokha zonsezi. Nanga bwanji mukuyankhula zopanda pake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, inu nonse munaciona; Ndipo mugwidwa nazo zopanda pace cifukwa ninji?