Job 27:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Chilango chimene Mulungu amasungira munthu woipa, choloŵa chimene munthu wozunza anzake amalandira kwa Mphambe ndi ichi:
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ili ndi gawo la munthu woipa kwa Mulungu, ndi cholowa cha akupsinja anzao achilandira kwa Wamphamvuyonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pano pali chilango chimene Mulungu amasungira woyipa, cholowa chimene munthu wankhanza amalandira kuchokera kwa Wamphamvuzonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ili ndi gawo la munthu woipa kwa Mulungu, Ndi colowa ca akupsinja anzao acilandira kwa Wamphamvtiyonse.