Job 27:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ana ake ngakhale achuluke chotani, adzaphedwa ndi lupanga, zidzukulu zake zidzasoŵa chakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akachuluka ana ake, ndiko kuchulukira lupanga, ndi ana ake sadzakhuta chakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Angakhale ana ake achuluke chotani adzaphedwa ndi lupanga ndipo zidzukulu zake zidzasowa zakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akacuruka ana ace, ndiko kucurukira lupanga, Ndi ana ace sadzakhuta cakudya.