Job 27:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale aunjike siliva ngati fumbi, kapena kukundika zovala ngati mchenga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chinkana akundika ndalama ngati fumbi, ndi kukonzeratu zovala ngati dothi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale aunjike siliva ngati fumbi, ndi kukundika zovala ngati mchenga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cinkana akundika ndalama ngati pfumbi, Ndi kukonzeratu zobvala ngati dothi;