Job 27:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma olungama ndiwo amene adzavala zimenezo, ndipo anthu osachimwa adzagaŵana siliva ameneyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
azikonzeretu, koma wolungama adzazivala, ndi wosalakwa adzagawa ndalamazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
zimene wasungazo wolungama ndiye adzavale, ndipo anthu osalakwa ndiwo adzagawane siliva wakeyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Azikonzeretu, koma wolungama adzazibvala, Ndi wosalakwa adzagawa ndalamazo.